Pitani ku nkhani yake

Kumasulira Mabaibulo Osiyanasiyana

Mfundo Zimene Anatsatira Pomasulira Baibulo

Pomasulira Baibulo la Dziko latsopano, anatsatira mfundo 5 zikuluzikulu.

Dzina la Mulungu Limapezekanso mu Mpukutu Wakale

Onani umboni wosonyeza kuti dzina la Mulungu linkapezeka mu “Chipangano Chatsopano.”

Tapatsidwa Ntchito Yomasulira “Mawu Opatulika a Mulungu”​—Aroma 3:2

Kwa zaka zambiri, a Mboni za Yehova akhala akugwiritsira ntchito Mabaibulo osiyanasiyana. Koma n’chifukwa chiyani anaganiza zomasulira Baibulo m’Chingelezi chimene anthu amalankhula masiku ano?